0% found this document useful (0 votes)
14 views3 pages

BT Idp Joint Imams Monthly Contribution Program 2

This document outlines the details of a monthly contribution program between six selected imams from different areas in Malawi. The program consists of seven parts: (1) each imam is expected to contribute MK50,000 within 24 hours of the due date each month; (2) consequences for imams who fail to contribute include repayment or loss of stipend; (3) accommodations for imams unable to contribute; (4) a list of participating imams and their contact details; (5) the names of imams expected to receive the funds for the month; and (6) confirmation of the six imams available for the current meeting.

Uploaded by

Arabi Alee
Copyright
© © All Rights Reserved
We take content rights seriously. If you suspect this is your content, claim it here.
Available Formats
Download as PDF, TXT or read online on Scribd

You are on page 1/ 3

BT IDP JOINT IMAMS MONTHLY CONTRIBUTION PROGRAM

Malamulo ndi mfundo zili mmusinzi zalembedwa ndi kuunikidwa bwino ndi maimam onse
asanu mmodzi omwe asankha kupanga nawo programuyi

 Maimam asanu ochokera ku Blantyre

 Imam mmodzi ochokera kumwanza tonse ngati 6

Date:17th May 2023(Lachitatu kuambira 8:30pm-9:30pm)

MFUNDO NDI MALAMULO OENDESERA PROGRAMUYI

GAWO A:NDALAMA YOSONKHEDWA

 Imam aliense aenera kumapereka ndalama yokwana K50,000

 Ndalama iyenera kuperekedwa pasanaduse 24hrs (tsiku limodzi)
 Ndalama iyenera kutumizidwa ku account yamunthu olandira mmwedzi umenewo

GAWO B:IMAM OKANIKA KUTSATIRA MFUNDO ZAMSONKHOMSONKHO

Imam yemwe adzakanike kubwedza ndalama yoti iye walandira kale mfundo izi zizatsatidwa

 Imam otere azafunsidwa zifukwa zomwe zamupangisa kutero

 Imam otere mwapadera adzaenera kuyenderedwa kumalo ake antchito olo
kukadandaulidwa kuoffice yake
 Imam otere adzaenera kupangidwa report kuoffice ya idp kuti isamupase stipend
yake.

GAWO C:IMAM NGATI ATAMWALIRA MUNTHAWI YOSONKHAYI

Muchifuniro cha Allah ngati imam watisia munyengo yosonkhayi.mfundo zotsatirazi

zizatsatidwa

 Ndalama yomwe adatenga idzaenera kubwezedwa kudzera kuidp/stipend

 Kapena idzaenera kuchoseredwa ngati maimam amzake a idp angamusonkhere
ndalama yachipepeso
 Kapena maimam adzaenera kuthandizana kumubwezera imamuyu

GAWO D:IMAM NGATI WAKUMANA NDI VUTO MUNTHAWI YOMWE AKUFUNA

KUSONKHA

Ngati imam zamuvuta munthawi yomwe akufuna kusonkha azaenera kutsatira mfundo izi:

 Choamba adzaenera kulumikizana ndi munthu olandira wamwedzi umenewo

 Olandira ngati sadakhutire ndi dandaulo lamzakelo azaenera kudziwisa gulu
 Ngati mchitidwe uzaoneke kuti mchizolowedzi chaimam, imam otere
sadzaloledwanso kulowa nawo mgululi mu phase ina.
GAWO E:MAINA AMAIMAM OMWE ALI MAMEMBALA AGULULI

NO IMAMS NAME AREA ORG GUARDIAN OFFICE NO IMAMS NO

1. ABDUL RASHEED ALABI BT 0993557909 0994742642 0882795825
2. RAJAB MAKANDE BT BENA 0881240619 0994383961 0881407669
C.T
3. ABDUL AZIZ BALUTI BT 0881921860 0882704665
4. SHARIF MAULANA BT MAM 0999447652 0999856926 0888885234
5. RIDHWAN MOENDA MZ IFFD 0990276417 0888222225 0994605675
6. ABDULLAH ATIBA BT 0734188913 0888314000 0880936651

GAWO F:MAINA AMAIMAM OMWE AYAMBIRE KULANDIRA

NO IMAMS NAME AREA

1. ABDUL RASHEED ALLI KACHERE
2. SHAREEF MAULANA MADZIABANGO
3. ABDUL AZIZ BALUTI KACHERE
4. ABDULLAH ATIBA LUNZU
5. RAJAB MAKANDE CHILEKA
6. RIDHWAAN MOENDA MWANZA

GAWO G:MAIMAM OMWE ADAPEZEKA PAMKUMANOWO

 SH ABDUL RASHEED ALABI

 SH RAJAB MAKANDE
 SH ABDUL AZIZ BALUTI
 SH SHARIF MAULANA
 SH RIDHWAN MOENDA
 SH ABDULLAH ATIBAH

You might also like